About Tikudzala Mitengo
Ku Malawi kusakhale mbe mbe mbe. Tiyeni tidzale mitengo pamakhomo, kuminda, kumasitolo, kumanda, mumjira. Paliponsepo. Ine mitengo yanga yakumalawi ndidadzala mumpoto. dzalani. dzinthunzi ndipo tionetseni Pano. zikomo kwambiri azibale anga.xx